Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Taonani! Mdani adzabwera ngati mitambo yamvula ndipo magaleta* ake ali ngati mphepo yamkuntho.+ Mahatchi* ake ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga.+ Tsoka ife chifukwa tafunkhidwa.

  • Maliro 4:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Otithamangitsawo ndi aliwiro kuposa ziwombankhanga zouluka m’mwamba.+

      Iwo atithamangitsa pamapiri.+ Atibisalira m’chipululu.+

  • Ezekieli 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ku Lebanoni+ kunabwera chiwombankhanga chachikulu+ chokhala ndi mapiko aakulu+ ndi aatali. Chiwombankhangacho chinali ndi nthenga zambiri zamitundu yosiyanasiyana. Chitafika kumeneko, chinathyola nsonga ya mtengo+ wa mkungudza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena