Yesaya 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mivi yawo ndi yakuthwa ndipo mauta awo onse ndi okungika.+ Ziboda za mahatchi awo n’zolimba ngati mwala wa nsangalabwi.+ Mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+
28 Mivi yawo ndi yakuthwa ndipo mauta awo onse ndi okungika.+ Ziboda za mahatchi awo n’zolimba ngati mwala wa nsangalabwi.+ Mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+