Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho ngakhale mwamuna wolimba mtima amene ali ndi mtima ngati wa mkango+ adzafooka+ ndithu. Izi zili choncho chifukwa Isiraeli yense akudziwa kuti bambo wako ndi mwamuna wamphamvu,+ ngatinso mmene alili amuna olimba mtima amene ali naye.+

  • Miyambo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+

  • Yesaya 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti Yehova wandiuza kuti: “Mkango umalira moopseza, ngakhale mkango wamphamvu,+ poteteza nyama imene wagwira. Abusa ambirimbiri akaitanidwa kuti adzauthamangitse, ngakhale umve mawu awo suchita mantha ndipo ngakhale azichita phokoso suopa. M’njira yomweyo, Yehova wa makamu adzatsika kuti achite nkhondo poteteza phiri la Ziyoni ndiponso poteteza phiri lake laling’ono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena