8 Ndiyeno Husai anapitiriza kunena kuti: “Iwe ukuwadziwa bwino bambo wako ndi amuna amene ali nawo kuti iwo ndi amphamvu+ ndipo mitima ikuwapweteka+ ngati chimbalangondo chimene chataya ana ake kuthengo.+ Ukudziwanso bwino kuti bambo wako ndi munthu wankhondo+ ndipo sangagone kumene kuli anthu.