Oweruza 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo ana a Dani anamuuza kuti: “Usayandikire kuno ndipo tisamvenso mawu akowo, chifukwa anthu olusa+ angakupwetekeni, ndipo iweyo ungataye moyo wako ndi kutayitsa moyo wa anthu a m’nyumba yako.”
25 Pamenepo ana a Dani anamuuza kuti: “Usayandikire kuno ndipo tisamvenso mawu akowo, chifukwa anthu olusa+ angakupwetekeni, ndipo iweyo ungataye moyo wako ndi kutayitsa moyo wa anthu a m’nyumba yako.”