2 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+ Miyambo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+ Hoseya 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+
24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+
12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+
8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa+ ndipo ndidzang’amba zifuwa zawo, mmene muli mitima yawo. Ndidzawadya kumeneko ngati mkango.+ Chilombo chakuthengo chidzawakhadzulakhadzula.+