Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Choncho Davide, mwa kugwiritsa ntchito gulaye ndi mwala, anali wamphamvu kuposa Mfilisiti. Iye anamukantha ndi kumupha, ndipo m’manja mwa Davide munalibe lupanga.+

  • 1 Samueli 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:

      “Sauli wakantha adani ake masauzande,

      Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+

  • 1 Samueli 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Patapita nthawi, nkhondo inayambanso ndi Afilisiti. Davide anapita kukamenya nkhondoyo ndipo anakantha ndi kupha Afilisiti ochuluka,+ moti Afilisitiwo anathawa pamaso pake.+

  • 2 Samueli 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Asiriyawo anathawa+ pamaso pa Isiraeli, ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta,+ ndi asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anakanthanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya, moti anafera pomwepo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena