Deuteronomo 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+ Salimo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+
2 Yehova Mulungu wako adzawapereka ndithu kwa iwe ndipo udzawagonjetse.+ Udzawawononge ndithu+ ndipo usadzachite nawo pangano kapena kuwakomera mtima.+
3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+