1 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+ 1 Samueli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+ Miyambo 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Maso+ owala amapangitsa mtima kusangalala.+ Uthenga+ wabwino umanenepetsa mafupa.+
11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+
5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+