1 Samueli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+ 1 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+
7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+
11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+