1 Samueli 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+ 1 Samueli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+
7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:“Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+
5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+