1 Samueli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi ameneyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo kwinaku akuvina nʼkumati: ‘Sauli wapha adani ake masauzande,Ndipo Davide wapha masauzande ambirimbiriʼ?”+
5 Kodi ameneyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo kwinaku akuvina nʼkumati: ‘Sauli wapha adani ake masauzande,Ndipo Davide wapha masauzande ambirimbiriʼ?”+