1 Samueli 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+
5 Kodi uyu si Davide uja amene ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina n’kumati, ‘Sauli wakantha adani ake masauzande, ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+