Salimo 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho moyo wanga ukukondwera, ndipo ndidzakhala wosangalala.+Komanso ndidzakhala wotetezeka.+ Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+