Deuteronomo 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma inu simunafune kupita kukalowa m’dzikolo,+ ndipo munayamba kupandukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.+ 1 Samueli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngati mudzaopa Yehova,+ n’kumutumikiradi+ ndi kumvera mawu ake,+ ndipo ngati simudzapandukira+ malamulo a Yehova, Yehova Mulungu wanu adzakhala nanu, inuyo pamodzi ndi mfumu yokulamuliraniyo. Salimo 111:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chiweruzo.+נ [Nun]Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+
26 Koma inu simunafune kupita kukalowa m’dzikolo,+ ndipo munayamba kupandukira lamulo la Yehova Mulungu wanu.+
14 Ngati mudzaopa Yehova,+ n’kumutumikiradi+ ndi kumvera mawu ake,+ ndipo ngati simudzapandukira+ malamulo a Yehova, Yehova Mulungu wanu adzakhala nanu, inuyo pamodzi ndi mfumu yokulamuliraniyo.
7 Ntchito za manja ake zimadziwika ndi choonadi ndiponso chiweruzo.+נ [Nun]Malamulo onse amene amapereka ndi odalirika.+