Deuteronomo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu. Miyambo 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+ Mateyu 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma iye anawayankha kuti: “N’chifukwa chiyani inunso mumaphwanya malamulo a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu?+
6 “Tsopano amenewa ndiwo malamulo, malangizo ndi zigamulo zimene Yehova Mulungu wanu walamula kuti ndikuphunzitseni,+ kuti muzikazitsatira m’dziko limene mukuwolokerako kukalitenga kukhala lanu.
4 Bambo anga anali kundilangiza+ kuti: “Mtima wako+ ugwire mwamphamvu mawu anga.+ Sunga malamulo anga kuti upitirize kukhala ndi moyo.+
3 Koma iye anawayankha kuti: “N’chifukwa chiyani inunso mumaphwanya malamulo a Mulungu chifukwa cha miyambo yanu?+