Salimo 33:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti mawu a Yehova ndi owongoka,+Ndipo ntchito zake zonse ndi zodalirika.+