Salimo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+
15 Maso anga amayang’ana kwa Yehova nthawi zonse,+Chifukwa iye ndi amene amawonjola phazi langa mu ukonde.+