Oweruza 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pambuyo pa Ehudi panadzakhala Samagara+ mwana wamwamuna wa Anati. Ameneyu anapha amuna achifilisiti+ 600 ndi chisonga chotosera ng’ombe pozitsogolera. Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.+ Oweruza 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zitatero, anapeza fupa laliwisi la nsagwada za bulu wamphongo, n’kukantha nalo amuna 1,000.+ 1 Samueli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiye zinali kuchitika kuti, pa tsiku lankhondo panalibe munthu aliyense mwa anthu amene anali ndi Sauli ndi Yonatani, amene anali ndi lupanga+ kapena mkondo m’manja mwake. Koma Sauli+ yekha ndi mwana wake Yonatani ndi amene anali ndi zida. 1 Samueli 17:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+
31 Pambuyo pa Ehudi panadzakhala Samagara+ mwana wamwamuna wa Anati. Ameneyu anapha amuna achifilisiti+ 600 ndi chisonga chotosera ng’ombe pozitsogolera. Ameneyunso anapulumutsa Isiraeli.+
22 Ndiye zinali kuchitika kuti, pa tsiku lankhondo panalibe munthu aliyense mwa anthu amene anali ndi Sauli ndi Yonatani, amene anali ndi lupanga+ kapena mkondo m’manja mwake. Koma Sauli+ yekha ndi mwana wake Yonatani ndi amene anali ndi zida.
47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+