Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Dziko limene ndidzakupatsa lidzayambira ku Nyanja Yofiira mpaka kunyanja ya Afilisiti, ndiponso kuyambira kuchipululu mpaka ku Mtsinje.*+ Ndidzachita izi, chifukwa anthu okhala m’dzikomo ndidzawapereka m’manja mwako, ndipo iwe udzawathamangitsa pamaso pako.+

  • Yoswa 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Dziko limene latsala ndi ili:+ Madera onse a Afilisiti+ ndi madera onse a Agesuri.+

  • Oweruza 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Samisoni anawauza kuti: “Ulendo uno ndilibe mlandu ndi Afilisiti ngati ndingachite zinthu zowavulaza.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena