1 Mbiri 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Asiriyawo anathawa+ pamaso pa Isiraeli, ndipo Davide anapha Asiriya 7,000 okwera magaleta, ndi asilikali 40,000 oyenda pansi. Komanso anapha Sofaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo.+
18 Koma Asiriyawo anathawa+ pamaso pa Isiraeli, ndipo Davide anapha Asiriya 7,000 okwera magaleta, ndi asilikali 40,000 oyenda pansi. Komanso anapha Sofaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo.+