1 Mbiri 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yowabu ndi amuna amene anali naye anapita kukamenyana ndi Asiriya,+ ndipo Asiriyawo anathawa+ pamaso pake. Salimo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+
14 Choncho Yowabu ndi amuna amene anali naye anapita kukamenyana ndi Asiriya,+ ndipo Asiriyawo anathawa+ pamaso pake.
16 Palibe mfumu imene inapulumuka chifukwa cha kukula kwa gulu lake lankhondo.+Munthu wamphamvu sapulumuka chifukwa cha kuchuluka kwa mphamvu zake.+