1 Mbiri 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Yowabu ndi amuna amene anali naye anapita kukamenyana ndi Asiriya ndipo Asiriyawo anayamba kuthawa.+
14 Kenako Yowabu ndi amuna amene anali naye anapita kukamenyana ndi Asiriya ndipo Asiriyawo anayamba kuthawa.+