Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 1:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tipite kuti? Abale athu achititsa mantha mitima yathu+ potiuza kuti: “Kumeneko tinaonako anthu akuluakulu, ndiponso aatali kuposa ifeyo,+ ndi mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri yofika kumwamba.+ Kumeneko tinaonakonso ana a Anaki.”’+

  • Yoswa 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo iye anauza amunawo kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani ndithu dziko lino.+ Ife tagwidwa ndi mantha chifukwa cha inu,+ ndipo anthu a dziko lino ataya mtima chifukwa chokuopani.+

  • Yoswa 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo amuna a ku Aiwo anapha amuna achiisiraeli pafupifupi 36. Anawathamangitsabe+ kuchokera kuchipata mpaka ku Sebarimu, n’kupitiriza kuwapha mpaka pamalo otsetsereka. Zitatero, mitima ya Aisiraeli onse inasungunuka ndi mantha.+

  • 1 Samueli 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Sauli+ ndi Aisiraeli onse atamva mawu a Mfilisitiwa anaopsezedwa ndipo anachita mantha kwambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena