Levitiko 26:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+ Yesaya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 N’chifukwa chake anthu onse adzataya mtima, ndipo mitima ya anthu onse idzasungunuka.+
36 “‘Ndidzaika mantha m’mitima ya otsala pakati panu+ amene ali m’dziko la adani awo, moti adzathawa m’tswatswa wa tsamba louluka, ndipo adzathawa ngati kuti akuthawa lupanga. Pamenepo adzagwa popanda munthu wowathamangitsa.+