Chivumbulutso 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango.+ Chamoyo chachiwiri chinali ngati mwana wa ng’ombe wamphongo.+ Chamoyo+ chachitatu chinali ndi nkhope ngati ya munthu, ndipo chamoyo+ chachinayi chinali ngati chiwombankhanga+ chimene chikuuluka.
7 Chamoyo choyamba chinali ngati mkango.+ Chamoyo chachiwiri chinali ngati mwana wa ng’ombe wamphongo.+ Chamoyo+ chachitatu chinali ndi nkhope ngati ya munthu, ndipo chamoyo+ chachinayi chinali ngati chiwombankhanga+ chimene chikuuluka.