Ezekieli 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kachisiyo anali ndi zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza.+ Mtengo uliwonse wa kanjedza unali pakati pa akerubi awiri ndipo kerubi aliyense anali ndi nkhope ziwiri.
18 Kachisiyo anali ndi zithunzi zojambula mochita kugoba za akerubi+ ndi za mitengo ya kanjedza.+ Mtengo uliwonse wa kanjedza unali pakati pa akerubi awiri ndipo kerubi aliyense anali ndi nkhope ziwiri.