Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 6:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamakoma onse a nyumbayo, m’zipinda zonse ziwiri, chamkati ndi chakunja, anajambulapo akerubi,+ mitengo ya kanjedza,+ ndi maluwa.+ Anajambula zinthu zimenezi mochita kugoba.

  • 1 Mafumu 7:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Komanso pamalata a m’mbali mwa chokhazikapo besenicho, ndi pazitsulo zimene zinali pakati pa malatawo, anajambulapo mochita kugoba+ akerubi, mikango, ndi mitengo yakanjedza malinga ndi kukula kwa malo ake. Anajambulanso mochita kugoba nkhata zamaluwa kuzungulira chokhazikapo besenicho.+

  • 2 Mbiri 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo mitanda yake ya denga,* makomo, makoma,* ndi zitseko za nyumbayo anazikuta ndi golide.+ Pamakoma ake anajambulapo akerubi mochita kugoba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena