Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Utenge miyala iwiri ya onekisi+ ndi kulembapo+ mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba.+

  • Ekisodo 39:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno anakonza miyala ya onekisi+ ndi kuiika m’zoikamo zagolide. Pamiyalayo analembapo mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.+

  • Ekisodo 39:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.

  • 1 Mafumu 6:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Pamakoma onse a nyumbayo, m’zipinda zonse ziwiri, chamkati ndi chakunja, anajambulapo akerubi,+ mitengo ya kanjedza,+ ndi maluwa.+ Anajambula zinthu zimenezi mochita kugoba.

  • 1 Mafumu 6:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Zitseko ziwirizo zinali za matabwa a mtengo wa mafuta. Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa, ndipo anazikuta ndi golide. Kenako akerubi ndi mitengo ya kanjedza yolemba mochita kugoba ya pazitsekozo, anazikuta ndi golide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena