Ekisodo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Pamene Yakobo, kapena kuti Isiraeli anapita ku Iguputo, aliyense mwa ana ake aamuna anapitanso limodzi ndi banja lake. Mayina a ana a Yakobowo ndi awa:+ Ekisodo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Utenge miyala iwiri ya onekisi+ ndi kulembapo+ mayina a ana a Isiraeli mochita kugoba.+ Ekisodo 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayina 6 uwalembe pamwala umodzi ndipo mayina 6 otsalawo uwalembe pamwala winawo motsatira mmene anabadwira.+
1 Pamene Yakobo, kapena kuti Isiraeli anapita ku Iguputo, aliyense mwa ana ake aamuna anapitanso limodzi ndi banja lake. Mayina a ana a Yakobowo ndi awa:+
10 Mayina 6 uwalembe pamwala umodzi ndipo mayina 6 otsalawo uwalembe pamwala winawo motsatira mmene anabadwira.+