-
2 Mbiri 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho nditumizireni munthu waluso pa ntchito zagolide, zasiliva, zamkuwa,+ zachitsulo, ndiponso waluso pa ntchito za ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira ndi wabuluu. Munthuyo akhalenso wodziwa kujambula ndi kulemba mochita kugoba, kuti adzagwire ntchito pamodzi ndi anthu aluso amene ndili nawo kuno ku Yuda ndi ku Yerusalemu, omwe Davide bambo anga anawasankha.+
-