Ekisodo 39:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Miyalayo anaiika malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, ndipo inalipo 12, malinga ndi mayina awo. Mwala uliwonse analembapo mochita kugoba limodzi mwa mayina a mafuko 12, ngati mmene amagobera chidindo.+
14 Miyalayo anaiika malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, ndipo inalipo 12, malinga ndi mayina awo. Mwala uliwonse analembapo mochita kugoba limodzi mwa mayina a mafuko 12, ngati mmene amagobera chidindo.+