Ekisodo 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Miyalayo uiike malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, malinga ndi mayina a mafuko awo 12.+ Miyalayo ikhale yolembedwa mogoba ngati mmene amagobera chidindo, mwala uliwonse ukhale ndi limodzi mwa mayina a mafuko 12.+
21 Miyalayo uiike malinga ndi mayina a mafuko a ana a Isiraeli, malinga ndi mayina a mafuko awo 12.+ Miyalayo ikhale yolembedwa mogoba ngati mmene amagobera chidindo, mwala uliwonse ukhale ndi limodzi mwa mayina a mafuko 12.+