Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+ Levitiko 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose. Zekariya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Pa tsiku limenelo, pamabelu a mahatchi padzalembedwa mawu+ akuti ‘Chiyero n’cha Yehova!’+ Ndipo miphika yakukamwa kwakukulu+ ya m’nyumba ya Yehova adzaigwiritsa ntchito ngati mbale zolowa+ za paguwa lansembe.+
36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+
9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
20 “Pa tsiku limenelo, pamabelu a mahatchi padzalembedwa mawu+ akuti ‘Chiyero n’cha Yehova!’+ Ndipo miphika yakukamwa kwakukulu+ ya m’nyumba ya Yehova adzaigwiritsa ntchito ngati mbale zolowa+ za paguwa lansembe.+