Levitiko 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anamuvekanso nduwira+ kumutu kwake, nʼkuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
9 Anamuvekanso nduwira+ kumutu kwake, nʼkuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.