2 Mbiri 29:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo anapha+ ng’ombezo ndipo ansembe anatenga magazi+ ake n’kuwaza+ paguwa lansembe. Kenako anapha nkhosa zamphongo+ zija n’kuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja n’kuwaza magazi+ ake paguwa lansembe.
22 Iwo anapha+ ng’ombezo ndipo ansembe anatenga magazi+ ake n’kuwaza+ paguwa lansembe. Kenako anapha nkhosa zamphongo+ zija n’kuwaza magazi ake paguwa lansembe. Atatero anapha ana a nkhosa amphongo aja n’kuwaza magazi+ ake paguwa lansembe.