Levitiko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ena mwa magaziwo aziwapaka panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, m’chihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako. Aheberi 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo anawazanso magazi aja pachihema+ ndi paziwiya zonse zogwiritsa ntchito potumikira ena.+
5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
18 Ena mwa magaziwo aziwapaka panyanga za guwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova, m’chihema chokumanako. Magazi ena onse aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.