Ekisodo 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Upange guwa lansembe la zofukiza.+ Ulipange ndi matabwa a mthethe. Ekisodo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Guwalo uliike kutsogolo kwa nsalu yotchinga imene ili pafupi ndi likasa la umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni,* pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+
6 Guwalo uliike kutsogolo kwa nsalu yotchinga imene ili pafupi ndi likasa la umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni,* pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+