Ekisodo 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Guwalo uliike kutsogolo kwa katani imene ili pafupi ndi likasa la Umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni, pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+
6 Guwalo uliike kutsogolo kwa katani imene ili pafupi ndi likasa la Umboni.+ Likhale patsogolo pa chivundikiro chimene chili pamwamba pa Umboni, pomwe ndidzaonekera kwa iwe.+