Ekisodo 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kataniyi uipachike mʼmunsi mwa ngowe zolumikizira nsalu zapamwamba pa chihema, ndipo uike likasa la Umboni+ kuseri kwa kataniyi. Kataniyi ikhale malire a Malo Oyera+ ndi Malo Oyera Koposa.+ Aheberi 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+
33 Kataniyi uipachike mʼmunsi mwa ngowe zolumikizira nsalu zapamwamba pa chihema, ndipo uike likasa la Umboni+ kuseri kwa kataniyi. Kataniyi ikhale malire a Malo Oyera+ ndi Malo Oyera Koposa.+
3 Koma kuseri kwa nsalu yotchinga yachiwiri+ kunali chipinda chinanso chotchedwa “Malo Oyera Koposa.”+