Ekisodo 40:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno analowetsa tebulo+ mʼchihema chokumanako nʼkuliika kumbali yakumpoto ya chihemacho, kunja kwa katani. Ekisodo 40:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako anaika guwa lansembe lagolide+ mʼchihema chokumanako patsogolo pa katani,
22 Ndiyeno analowetsa tebulo+ mʼchihema chokumanako nʼkuliika kumbali yakumpoto ya chihemacho, kunja kwa katani.