Ekisodo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe+ masentimita 90 mulitali, masentimita 45 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi mpaka mʼmwamba.+ Aheberi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa panamangidwa chipinda choyamba cha chihema ndipo mʼchipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo ndi mikate yoonetsa kwa Mulungu,*+ ndipo chinkatchedwa “Malo Oyera.”+
10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe+ masentimita 90 mulitali, masentimita 45 mulifupi ndi masentimita 70 kuchoka pansi mpaka mʼmwamba.+
2 Chifukwa panamangidwa chipinda choyamba cha chihema ndipo mʼchipindamo munali choikapo nyale,+ tebulo ndi mikate yoonetsa kwa Mulungu,*+ ndipo chinkatchedwa “Malo Oyera.”+