Nehemiya 12:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zochuluka+ ndipo anasangalala+ pakuti Mulungu woona anawachititsa kusangalala kwambiri.+ Akazi+ ndi ana+ nawonso anasangalala, mwakuti phokoso la chisangalalo cha Yerusalemu linamveka kutali.+ Salimo 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+ Salimo 126:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 126 Pamene Yehova anasonkhanitsa ndi kubwezeretsa ogwidwa ukapolo a Ziyoni,+Tinakhala ngati tikulota.+ Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
43 Pa tsiku limenelo anapereka nsembe zochuluka+ ndipo anasangalala+ pakuti Mulungu woona anawachititsa kusangalala kwambiri.+ Akazi+ ndi ana+ nawonso anasangalala, mwakuti phokoso la chisangalalo cha Yerusalemu linamveka kutali.+
11 Inu olungama, kondwerani chifukwa cha zimene Yehova wachita ndipo sangalalani.+Fuulani ndi chisangalalo inu nonse owongoka mtima.+
126 Pamene Yehova anasonkhanitsa ndi kubwezeretsa ogwidwa ukapolo a Ziyoni,+Tinakhala ngati tikulota.+
10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+