Yesaya 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu a ku Ziyoni+ akadzabwerera n’kukakhala ku Yerusalemu,+ iwe sudzaliranso.+ Mosakayikira, iye adzakukomera mtima akadzamva kulira kwako. Akadzangomva kulira kwakoko, iye adzakuyankha.+ Yesaya 65:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+
19 Anthu a ku Ziyoni+ akadzabwerera n’kukakhala ku Yerusalemu,+ iwe sudzaliranso.+ Mosakayikira, iye adzakukomera mtima akadzamva kulira kwako. Akadzangomva kulira kwakoko, iye adzakuyankha.+
19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+