Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+ Yohane 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+ Yohane 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ngati anthu amene anatsutsidwa ndi mawu a Mulungu anawatcha ‘milungu,’+ ndipo Malemba satha mphamvu,+ Afilipi 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti iye anali ndi maonekedwe a Mulungu,+ kukhala wolingana ndi Mulungu sanakuganizirepo ngati chinthu choti angalande.+
6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+
18 Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse,+ mulungu wobadwa yekha+ amene ali pachifuwa+ cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu.+
35 Ngati anthu amene anatsutsidwa ndi mawu a Mulungu anawatcha ‘milungu,’+ ndipo Malemba satha mphamvu,+
6 Ngakhale kuti iye anali ndi maonekedwe a Mulungu,+ kukhala wolingana ndi Mulungu sanakuganizirepo ngati chinthu choti angalande.+