Yesaya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+ Yohane 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikusiyirani mtendere, ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu mmene dziko limauperekera ayi. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.
18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+
27 Ndikusiyirani mtendere, ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu mmene dziko limauperekera ayi. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.