Yohane 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndanena zimenezi kwa inu kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ M’dzikomu mukumana ndi masautso, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+ Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+ Afilipi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu. Akolose 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, mtendere+ wa Khristu ulamulire m’mitima+ yanu, popeza munaitanidwa ku mtenderewo monga ziwalo za thupi limodzi.+ Ndiponso, sonyezani kuti ndinu oyamikira. 2 Atesalonika 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Ambuye wamtendere mwiniyo, akupatseni mtendere nthawi zonse m’njira iliyonse.+ Ambuye akhale nanu nonsenu.
33 Ndanena zimenezi kwa inu kuti mukhale mu mtendere chifukwa cha ine.+ M’dzikomu mukumana ndi masautso, koma limbani mtima. Ine ndaligonjetsa dziko.”+
14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+
7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene umaposa kuganiza mozama kulikonse, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.
15 Komanso, mtendere+ wa Khristu ulamulire m’mitima+ yanu, popeza munaitanidwa ku mtenderewo monga ziwalo za thupi limodzi.+ Ndiponso, sonyezani kuti ndinu oyamikira.
16 Tsopano Ambuye wamtendere mwiniyo, akupatseni mtendere nthawi zonse m’njira iliyonse.+ Ambuye akhale nanu nonsenu.