Yohane 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndikusiyirani mtendere, ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu mmene dziko limauperekera ayi. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha. Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+
27 Ndikusiyirani mtendere, ndikupatsani mtendere wanga.+ Sindikuupereka kwa inu mmene dziko limauperekera ayi. Mitima yanu isavutike kapena kuchita mantha.
14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+