Yohane 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+ Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+ Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
14 Choncho Mawu ameneyo anakhala ndi thupi+ la nyama ndi kukhala pakati pathu, ndipo tinaona ulemerero wake, ulemerero wa mwana wobadwa yekha+ kwa bambo ake. Anali wodzaza ndi kukoma mtima kwakukulu ndi choonadi.+
16 “Pakuti Mulungu anakonda+ kwambiri dziko mwakuti anapereka Mwana wake wobadwa yekha,+ kuti aliyense wokhulupirira+ iye asawonongeke,+ koma akhale ndi moyo wosatha.+
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.