Miyambo 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Yehova anandipanga monga chiyambi cha njira yake.+ Ine ndiye ntchito yoyambirira pa ntchito zake zimene anakwaniritsa kalekale kwambiri.+ Akolose 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye ndiye chifaniziro+ cha Mulungu wosaonekayo,+ woyamba kubadwa+ wa chilengedwe chonse, Chivumbulutso 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+
22 “Yehova anandipanga monga chiyambi cha njira yake.+ Ine ndiye ntchito yoyambirira pa ntchito zake zimene anakwaniritsa kalekale kwambiri.+
14 “Kwa mngelo wa mpingo wa ku Laodikaya,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena Ame,+ mboni+ yokhulupirika+ ndi yoona,+ woyamba wa chilengedwe cha Mulungu.+